Kalombo ka COVID-19 kadwalitsa Anthu ambili osiyana siyana mu dziko lonse lapansi. Kagulu ka anthu aku chalo cha Canada uyanganila pali thandizo pakati ka anthu osauka afalitsa mbiri ya COVID-19 mu vitundu vosiyana siyana kulinganiza ndondomeko ya World Health Organization (WHO) no tantabuza mbiri yaba United Nations kuti mbiri iyi yifike konse.
Falitsani mbili imeneyi kugwilisa nchito wailesi, wailesi yaka nema, facebook kapena Whatsapp kuti ti thandize dziko lonse ku dziwa pali nthenda yi.
LetsStopAIDS is Canada's Youth-HIV charity, that inspires youth to take action, relating to HIV, within local communities. This website and its multilingual content was developed in 6 days by 65 volunteers from 13 countries (with $0).
To learn more about HeyCOVID19, view our Slide Deck.
Click here if you want to submit content in your language. If you spot an error, click here to let us know.
Please note: Information surrounding COVID-19 is constantly evolving. Please check with your local health authority and the WHO for up-to-date advice.