Chigobade kuvala?😷 kapena ayi?😮

Chigobade kuvala?😷 kapena ayi?😮
Download Image

Khodi mwadwala chifuwa kapena chimfine? Khodi simumvela bwino? Maka maka anthu omwe alangiza matenda a COVID-19 mu thupi wao.Sungani vigobade kuti anthu oyenera avigwilise nchito.

Choonadi

Kalombo ka COVID-19 kafalitsidwa kupyolera zotuluka mkamwa muntu akakhosola. Zichingilizeni paku talukana ndi anthu odwala ndiponso musagwile gwile vintu olo anthu odwala chosasamba ku manja mosilizila. Chigobade chithandizila kuti kalombo kasa falitsike mwamusanga paku chingiliza kugwila ku mphuno, kamwa ndi menso.

https://www.who.int/emergencies/diseases/novel-coronavirus-2019/advice-for-public/when-and-how-to-use-masks 
https://www.cdc.gov/coronavirus/2019-ncov/prevent-getting-sick/prevention.html