Akuda, osweta kapena azungu, tonse tili pachiopsezo chodwala nthendayi.

Akuda, osweta kapena azungu, tonse tili pachiopsezo chodwala nthendayi.
Download Image

Kalombo ka COVID-19 kalibe malile, ngankhale ana achichepele kapena achikulile, mitundu ya anthu osiyana siyana kapena ngati ali naka lombo ka HIV kapena aliye, aliyense angadwale nthendayi.

Choonadi

Kafalitsidwe ka COVID- 19 kabwela ndi ku zondana pakati a anthu amitundu zosiyana siyana. Tiyeni tikumbuke mumene matenda osiyana siyana yanagwela dziko lonse ndipo mwamene anthu ana nzunzika ndi matenda aya. Tiyeni ti falitse mbili yachikondi ku anthu ku pyolera zochitika ndi makambidwe yathu.

News Source:
https://www.theatlantic.com/international/archive/2020/03/coronavirus-covid19-xenophobia-racism/607816/