Agogo. Amai. Amalume. Mwana. Tonse ndife amodzi pakati pa nthenda iyi!

Agogo. Amai. Amalume. Mwana. Tonse ndife amodzi pakati pa nthenda iyi!
Download Image

Kulangiza CHIFUNDO ndi chinthu chabwino, sungani anzanu mwachikondi ndiponso kulinganiza pakati pa anthu.

Choonadi

Munthu aliyense angatenge Kalombo ka COVID-19. Komanso, anthu achikulile ndi aja omwe ali nthenda zina zache zilizonse monga kalombo ka HIV, kapena anthu asaliwa nthanzi bali pachiopsezo chotengela kalombo aka.

https://www.who.int/news-room/q-a-detail/q-a-on-covid-19-hiv-and-antiretrovirals