Mbiri ya boza ya COVID-19. Mankwala achiboyi, moba kapena mankwala ena aliyonse siya chilisa kalombo ka COVID-19.

Mbiri ya boza ya COVID-19. Mankwala achiboyi, moba kapena mankwala ena aliyonse siya chilisa kalombo ka COVID-19.
Download Image

Kalombo ka COVID-19 sikayenda nampepo! Kumwa moba siku paya COVID-19. Kulibe mankwala yo chilitsa ndipo kulibe mukwala yo poletsa.

‍

Choonadi

Kufalisa moba pa thupi,  kumwa chlorine kapena kusheta mankwala yachiboyi siku ngaphe kalombo ka COVID-19. COVID-19 ifalitsidwa ndi chimfine , mata yotuluka paja munthu ali na kalombo akakhosola kapena po kamba. Tiyeni tisambe 👐 ndi kusamala manja athu ndiponso tiyeni tisagwile gwile menso, mphuno ndi kamwa 👀👃👄.

‍

https://www.who.int/emergencies/diseases/novel-coronavirus-2019/advice-for-public/myth-busters‍
https://www.instagram.com/p/B-UieTUD42A