Njira yoyambila: sambani mmanja na soap ndi madzi yotuba Njira Yachiwiri: Bwezaniponi njira yoyamba 😜

Njira yoyambila: sambani mmanja na soap ndi madzi yotuba Njira Yachiwiri: Bwezaniponi njira yoyamba 😜
Download Image

Manja yanu ni malo oyamba ponkhala kalombo ka COVID-19. Tiyeni tisamale manja athu kupyolera kusuka na soap ndi madzi pa nthawi mphindi makhumi yawiri.

‍

Choonadi

Njira zisanu mosukila mmanja (βœ‹). ‍

Sambani mmanja pa thanwi ya mpindi makhumi awiri, ngati sitelo, gwilisani nchito hand sanitizer ili na 60% moba. Valani mphuno ndi kamwa po khosola ndi kamboyo, osati manja. Osagwila menso, kamwa kapena mphuno. Talukani pakati kaanthu,makamaka baja ali na nthenda ya chifuwa. Nkhalani pa nyumba.

‍

Kalombo ka COVID-19 kankala pa zintu zosiya mu nthawi ya maola 72. Β Njira izi zisanu zizateteza inu ku kalombo ka COVID-19.

‍

https://www.cdc.gov/coronavirus/2019-ncov/prevent-getting-sick/prevention.html