Ngati mudela nkhawa, #nkalani panyumba

Ngati mudela nkhawa, #nkalani panyumba
Download Image

Ngati mumvela kudwala, chifuwa, kapena kuchepekela kwa mpweya. Pitani kuchipatala. Ngati kulibe zo langiza pa thupi kuti muli na nthenda ya COVID-19, munga falitse kalombo.

Choonadi

Kudwala, kulema kwa thupi, chifuwa chosasila nakuvutika kufuza ni zilangizo za nthenda ya COVID-19 mu thupi. Zilangizo zina ni Kuthurula, Thupi kubaba na chifuwa chofwasa. Nichoyenera kwambiri kuziba kuti sibonse bodwala COVID-19 azalangiza pa thupi kuti ali naka lombo.

https://www.who.int/news-room/q-a-detail/q-a-coronaviruses