Zig’ono ni Zambiri #KhalaniPanyumba #MwekaTonse

Zig’ono ni Zambiri #KhalaniPanyumba #MwekaTonse
Download Image

Choyambilapo, Zisamalileni. Chokonkapo, tiyeni tisamalile ndiponso kuthandiza Anzathu omwe ayenekera thandizo. Chosilizila, Nkalani panyumba iyi ndiye Njira imodzi yopewa kalombo ka COVID-19.

Choonadi

Zisamilileni ndiponso pelekani thandizo kuli anthu ena. Kuthandizirana ni chinthu chaphindu kuli aliyense. Mwachisanzo, Tumilani phone anzanu omwe afunika thandizo. Kusebenzela pamodzi kwati banja limodzi kuthandizira kwambiri kuphewa kalombo ka COVID-19.

https://www.who.int/docs/default-source/coronaviruse/mental-health-considerations.pdf
https://www.gfmer.ch/Medical_search/Ministry_health.html