Nichabwino ku tuma message kuchila kunkala bama dandaulo

Nichabwino ku tuma message kuchila kunkala bama dandaulo
Download Image

Kutalukana sikuthanthauza ⬅️ ➡️kuti chikondwelelo chisile. Munga pitiize kusangalala 🍑💕🍆 ndi okondedwa anu pa nthawi imodzi musamalilana.

Choonadi

Yetsetsani kusangalala patali ndi okondedwa  anu. Munga gwilise nchito phone kutuma vithunzi thunzi kapena video calling mwachilolezo. Ngati mwankala malo amozi ndi okondedwa anu, kumbukani ku gwilisa nchito condom ndiponso osalephela kumwa mankwala yanu ya PrEP kapena yakalombo ka HIV.

http://www.euro.who.int/en/health-topics/health-emergencies/coronavirus-covid-19/novel-coronavirus-2019-ncov-technical-guidance/stay-physically-active-during-self-quarantine/_recache%23article
https://www.unaids.org/en/resources/infographics/hiv-and-covid-19