Khodi muli naka lombo ka HIV? Kodi simuziba za Covid 19?🤔 Nkalani ozibisidwa!

Khodi muli naka lombo ka HIV? Kodi simuziba za Covid 19?🤔 Nkalani ozibisidwa!
Download Image

Khodi muli naka lombo ka HIV chiopsyezo chotenga ka lombo ka COVID-19 ndi chimozimozi. Ngati simunamwe mankwala yakalombo ka HIV, chiopsyezo chotenga COVID-19 chichuluka.

Choonadi

Ngati muli pa mankwala ya kalombo ka HIV, chiopsyezo chotenga ka lombo ka COVID-19 nichimozi mozi nabaja bantu aliye kalombo ka HIV. Ngati simunamwe mankwala yakalombo ka HIV, chiopsyezo chotenga COVID-19 chichuluka.

https://www.who.int/news-room/q-a-detail/q-a-on-covid-19-hiv-and-antiretrovirals